Genesis 49:2 - Buku Lopatulika2 Sonkhanani, tamvani, ana aamuna a Yakobo; tamverani Israele atate wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Sonkhanani, tamvani, ana amuna a Yakobo; tamverani Israele atate wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Bwerani kuno, ndipo mumve, inu ana a Yakobe, mverani bambo wanu Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Bwerani ndipo imvani mawu anga, inu ana a Yakobo; mverani abambo anu Israeli. Onani mutuwo |