Genesis 48:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo ine ndakupatsa iwe gawo limodzi loposa la abale ako, limene ndinalanda m'dzanja la Aamori ndi lupanga langa ndi uta wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo ine ndakupatsa iwe gawo limodzi loposa la abale ako, limene ndinalanda m'dzanja la Aamori ndi lupanga langa ndi uta wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ndiponso iweyo, osati abale ako, ndikukupatsa Sekemu, dera lija limene ndidachita cholanda ndi lupanga langa ndi uta wanga kwa Aamori.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndiponso iwe wekha ndikupatsa moposera abale ako, malo woonjezera, Sekemu, malo amene ndinalanda kwa Aamori ndi lupanga ndi uta wanga.” Onani mutuwo |