Genesis 48:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Israele anati kwa Yosefe, Taona, ndilinkufa ine; Mulungu adzakhala ndi iwe, adzakubwezanso iwe ku dziko la makolo ako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Israele anati kwa Yosefe, Taona, ndilinkufa ine; Mulungu adzakhala ndi iwe, adzakubwezanso iwe ku dziko la makolo ako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pambuyo pake Yakobe adauza Yosefe kuti, “Ukuwonatu kuti ndili pafupi kufa, koma Mulungu adzakhala nawe, ndipo adzakubweza ku dziko la makolo ako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kenaka Israeli anati kwa Yosefe, “Ine ndatsala pangʼono kufa, koma Mulungu adzakhala ndipo adzakutenganinso kubwerera nanu ku dziko la makolo anu. Onani mutuwo |