Genesis 48:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Yosefe anati kwa atate wake, Msatero atate wanga, chifukwa uyu ndi woyamba; ikani dzanja lanu lamanja pamutu wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Yosefe anati kwa atate wake, Msatero atate wanga, chifukwa uyu ndi woyamba; ikani dzanja lanu lamanja pa mutu wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adauza bambo wake kuti, “Musatero atate. Wamkulu ndi uyu. Dzanja lanu lamanja likhale pamutu pa ameneyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 nati kwa abambo ake, “Ayi, abambo anga, uyu ndiye woyamba kubadwa, ikani dzanja lanu lamanja pamutu pake.” Onani mutuwo |