Genesis 47:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Atate wako ndi abale ako afika kwa iwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Atate wako ndi abale ako afika kwa iwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono Farao adauza Yosefe kuti, “Bambo wako pamodzi ndi abale ako abwera kwa iwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Farao anati kwa Yosefe, “Abambo ako ndi abale ako abwera kwa iwe. Onani mutuwo |