Genesis 47:4 - Buku Lopatulika4 Nati kwa Farao, Tafika kuti tikhale m'dzikomo; popeza palibe podyetsa zoweta za akapolo anu; pakuti njala yakula m'dziko la Kanani. Mulole tsopano akapolo anu akhale m'dziko la Goseni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Nati kwa Farao, Tafika kuti tikhale m'dzikomo; popeza palibe podyetsa zoweta za akapolo anu; pakuti njala yakula m'dziko la Kanani. Mulole tsopano akapolo anu akhale m'dziko la Goseni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Tabwera kudzakhala nao m'dziko muno bwana, chifukwa ku Kanani kuli njala yoopsa, kotero kuti kulibe ndi msipu womwe wodyetsa zoŵeta. Chonde bwana, mutilole tikakhale ku dziko la Goseni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ife tabwera kudzakhala kuno kwa kanthawi chifukwa njala yafika poopsa ku Kanaani motero kuti kulibe msipu wodyetsera ziweto. Ndiye bwana tiloleni kuti tikhale ku Goseni.” Onani mutuwo |