Genesis 47:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo anati, Undilumbirire ine; namlumbirira iye. Ndipo Israele anawerama kumutu kwa kama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo anati, Undilumbirire ine; namlumbirira iye. Ndipo Israele anawerama kumutu kwa kama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Yakobe adauzanso Yosefe kuti, “Lumbira pamaso panga kuti udzachitadi zimenezi.” Apo Yosefe adalumbiradi, ndipo Yakobe adaŵerama kumutu kwa bedi lake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Yakobo anati, “Lumbira kwa ine.” Yosefe analumbira kwa iye, ndipo Israeli anapembedza Mulungu atatsamira ndodo yake. Onani mutuwo |