Genesis 47:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo iwo anati, Watipulumutsa miyoyo yathu; tipeze ufulu pamaso pa mbuyanga, ndipo tidzakhala akapolo a Farao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo iwo anati, Watipulumutsa miyoyo yathu; tipeze ufulu pamaso pa mbuyanga, ndipo tidzakhala akapolo a Farao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Anthu adayankha kuti, “Mwapulumutsa moyo wathu. Mwatichitira zabwino bwana, tidzakhala akapolo a Farao.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Iwo anati, “Mwatipulumutsa potichitira zabwinozi, mbuye wathu, tsono tidzakhala akapolo a Farao.” Onani mutuwo |