Genesis 47:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Yosefe anati, Mundipatse ng'ombe zanu: ndipo ndidzakupatsani inu mtengo wa ng'ombe zanu ngati ndalama zatsirizika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Yosefe anati, Mundipatse ng'ombe zanu: ndipo ndidzakupatsani inu mtengo wa ng'ombe zanu ngati ndalama zatsirizika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Yosefe adaŵayankha kuti “Bwerani ndi zoŵeta zanu, tidzasinthane ndi chakudya, ngati mukuti ndalama zanu zidatha zonse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo Yosefe anawayankha kuti, “Bwerani ndi ziweto zanu ndipo tidzasinthana ndi chakudya poti mukuti ndalama zanu zatha.” Onani mutuwo |