Genesis 46:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Mulungu ananena kwa Israele, m'masomphenya a usiku, nati, Yakobo, Yakobo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Mulungu ananena kwa Israele, m'masomphenya a usiku, nati, Yakobo, Yakobo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Usiku Mulungu adaonekera Israele m'masomphenya, ndipo adati, “Yakobe, Yakobe!” Iye adayankha kuti, “Ee Ambuye!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo Mulungu anayankhula ndi Israeli mʼmasomphenya usiku nati, “Yakobo! Yakobo!” Iye anayankha, “Ee, Ambuye.” Onani mutuwo |