Genesis 45:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Mulungu anatumiza ine patsogolo panu kuti ndikhazike inu mutsale m'dziko lapansi, ndi kusunga inu amoyo ndi chipulumutso chachikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Mulungu anatumiza ine patsogolo panu kuti ndikhazike inu mutsale m'dziko lapansi, ndi kusunga inu amoyo ndi chipulumutso chachikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mulungu adanditumiziratu ine kuno kuti ndikupulumutseni, kuti choncho ziwoneke zidzukulu zanu zambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma Mulungu ananditsogoza kuti adzakusungeni ndi moyo ndi kuti mudzakhale ndi zidzukulu pa dziko lapansi. Onani mutuwo |