Genesis 45:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anagwa pakhosi pake pa Benjamini, nalira; ndipo Benjamini nalira pakhosi pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anagwa pakhosi pake pa Benjamini, nalira; ndipo Benjamini nalira pakhosi pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Atatero adakumbatira Benjamini, mng'ono wake uja, nayambanso kulira. Benjamini nayenso adayamba kulira atangomkumbatira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Kenaka Yosefe anakhumbatira Benjamini, mngʼono wake uja nayamba kulira. Nayenso Benjamini anayamba kulira atamukumbatira. Onani mutuwo |