Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 45:12 - Buku Lopatulika

12 Taonani, maso anu aona, ndi maso a mphwanga Benjamini, kuti ndi m'kamwa mwanga ndilikulankhula ndi inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Taonani, maso anu aona, ndi maso a mphwanga Benjamini, kuti ndi m'kamwa mwanga ndilikulankhula ndi inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Tsono nonsenu ndi Benjamini, mng'ono wangayu, mungathe kuwona kuti ndinedi amene ndikulankhula nanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “Tsono inu nonse pamodzi ndi mʼbale wangayu Benjamini, mukuona kuti ndi inedi amene ndikuyankhula nanu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 45:12
5 Mawu Ofanana  

Ndipo sanadziwe kuti Yosefe anamva; chifukwa anali ndi womasulira.


ndipo ndidzachereza inu komweko; pakuti zatsala zaka zisanu za njala; kuti mungafikire umphawi, inu ndi banja lanu, ndi onse muli nao.


Ndipo mudzafotokozera atate wanga za ulemerero wanga wonse mu Ejipito, ndi zonse mwaziona; ndipo muzifulumira ndi kutsitsira kuno atate wanga.


Penyani manja anga ndi mapazi anga, kuti Ine ndine mwini: ndikhudzeni, ndipo penyani; pakuti mzimu ulibe mnofu ndi mafupa, monga muona ndili nazo Ine.


Pomwepo ananena kwa Tomasi, Bwera nacho chala chako kuno, nuone manja anga, ndipo bwera nalo dzanja lako, nuliike kunthiti yanga, ndipo usakhale wosakhulupirira, koma wokhulupirira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa