Genesis 44:34 - Buku Lopatulika34 Pakuti ndidzakwera bwanji kwa atate wanga, mnyamatayo akapanda kukhala ndi ine? Ndingaone choipa chidzagwera atate wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Pakuti ndidzakwera bwanji kwa atate wanga, mnyamatayo akapanda kukhala ndi ine? Ndingaone choipa chidzagwera atate wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Ine ndingathe bwanji kupita kwa bambo wanga popanda mnyamatayu kupita nane? Ine ndekha sindingathe kupirira kuti ndiwone tsoka lotere likugwera bambo wanga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ndingabwerere bwanji kwa abambo anga ngati sindingapite ndi mnyamatayu? Ayi! Sindifuna kukaona tsoka limene lingakagwere abambo anga.” Onani mutuwo |