Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 43:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo Israele anati, Chifukwa ninji munandichitira ine choipa chotero kuti munamuuza munthuyo muli ndi mphwanu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo Israele anati, Chifukwa ninji munandichitira ine choipa chotero kuti munamuuza munthuyo muli ndi mphwanu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Apo Israele adati, “Chifukwa chiyani mudathinitsa zinthu pa ine pomuuza kuti muli ndi mbale wanu winanso?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Tsono Israeli anafunsa kuti, “Bwanji inu munandiputira mavuto oterewa pomuwuza munthuyo kuti muli ndi mʼbale wanu wina?”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 43:6
3 Mawu Ofanana  

Koma mukapanda kumtuma iye sititsika; pakuti munthu uja anati kwa ife, Simudzaona nkhope yanga, ngati mphwanu sali ndi inu.


Ndipo iwo anati, Munthuyo anafunsitsa za ife, ndi za abale athu, kuti, Atate wanu alipo? Kodi muli ndi mphwanu? Ndipo tinamfotokozera iye monga mwa mau amenewo: ngati tinadziwa kuti iye adzati, Idzani naye mphwanu?


Ndipo anati kwa Mose, Kodi mwatichotsera kuti tikafe m'chipululu chifukwa panalibe manda mu Ejipito? Nchiyani ichi mwatichitira kuti mwatitulutsa mu Ejipito?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa