Genesis 43:13 - Buku Lopatulika13 mutengenso mphwanu, nimunyamuke, mupitenso kwa munthu uja: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 mutengenso mphwanu, nimunyamuke, mupitenso kwa munthu uja: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mtengeni mbale wanuyu, ndipo nyamukani, mupitenso kwa munthuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mutengeninso mngʼono wanuyu ndi kubwerera kwa munthuyo msanga. Onani mutuwo |