Genesis 42:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo anasenzetsa abulu ao tirigu wao nachokapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo anasenzetsa abulu ao tirigu wao nachokapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Abale akewo adasenzetsa abulu ao matumba a tirigu uja adagulayu, ndipo adanyamuka ulendo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Abale a Yosefe aja anasenzetsa abulu awo tirigu amene anagula uja ndipo ananyamuka ulendo wawo. Onani mutuwo |