Genesis 41:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo, taonani, ngala zisanu ndi ziwiri, zoonda zopserera ndi mphepo ya kum'mawa, zinamera pambuyo pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo, taonani, ngala zisanu ndi ziwiri, zoonda zopserera ndi mphepo ya kum'mawa, zinamera pambuyo pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kenaka padaphukanso ngala zina zisanu ndi ziŵiri zofwapa ndi zopserera ndi mphepo yamkuntho yakuvuma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kenaka ngala zina zisanu ndi ziwiri zinaphuka. Izi zinali zowonda ndi zowauka ndi mphepo ya kummawa. Onani mutuwo |