Genesis 41:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anagona nalotanso kachiwiri; ndipo taonani, ngala zisanu ndi ziwiri za tirigu zinamera pa mbuwa imodzi, zonenepa ndi zabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anagona nalotanso kachiwiri; ndipo taonani, ngala zisanu ndi ziwiri za tirigu zinamera pa mbuwa imodzi, zonenepa ndi zabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Atagonanso, adalota enanso maloto. Adaona ngala zatirigu zisanu ndi ziŵiri zitabala pa mphesi imodzi, ndipo zinali zakucha ndi zokhwima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Posakhalitsa anagonanso ndipo analota kachiwiri: Analota ngala zisanu ndi ziwiri za tirigu zathanzi labwino zitabala pa phata limodzi. Onani mutuwo |