Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 41:53 - Buku Lopatulika

53 Ndipo zaka zakuchuluka dzinthu zisanu ndi ziwiri za m'dziko la Ejipito, zinatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 Ndipo zaka zakuchuluka dzinthu zisanu ndi ziwiri za m'dziko la Ejipito, zinatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 Zaka zisanu ndi ziŵiri za dzinthu zitatha,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 Zaka zisanu ndi ziwiri za zokolola zochuluka zija zinatha,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 41:53
6 Mawu Ofanana  

Ndipo dzina la wachiwiri anamutcha Efuremu: chifukwa Mulungu anandibalitsa ine m'dziko la kusauka kwanga.


Ndipo zinayamba kufika zaka zisanu ndi ziwiri za njala, monga ananena Yosefe; ndipo munali njala m'maiko monse; koma m'dziko lonse la Ejipito munali chakudya.


Zaka ziwirizi muli njala m'dziko muno; ndipo zatsala zaka zisanu, zopanda kulima kapena kusenga.


Monga anthu atauka, apepula loto; momwemo, Inu Ambuye, pakuuka mudzapeputsa chithunzithunzi chao.


Koma Abrahamu anati, Mwana, kumbukira kuti unalandira zokoma zako pakukhala m'moyo iwe, momwemonso Lazaro zoipa; ndipo tsopano iye asangalatsidwa pano, koma iwe uzunzidwadi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa