Genesis 41:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo zaka zisanu ndi ziwiri zakuchuluka dzinthu nthaka inabala zambirimbiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo zaka zisanu ndi ziwiri zakuchuluka dzinthu nthaka inabala zambirimbiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Pa zaka zija za dzinthu dzambiri, m'dziko lonse munali chakudya chochuluka kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Mʼzaka zisanu ndi ziwiri za zokolola zambiri zija, anthu mʼdzikomo anakolola zochuluka. Onani mutuwo |