Genesis 41:33 - Buku Lopatulika33 Tsopano, Farao afunefune munthu wakuzindikira ndi wanzeru, amkhazike iye ayang'anire dziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Tsopano, Farao afunefune munthu wakuzindikira ndi wanzeru, amkhazike iye ayang'anire dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Tsopano inu mfumu sankhulani munthu wodziŵa zinthu ndi wanzeru, mumpatse ulamuliro pa dziko lonse la Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 “Tsopano Farao apezeretu munthu wozindikira ndi wanzeru ndipo amuyike kukhala woyangʼanira dziko lonse la Igupto. Onani mutuwo |