Genesis 41:23 - Buku Lopatulika23 ndipo, taona, ngala zisanu ndi ziwiri zina zofota, zoonda, zopserera ndi mphepo ya kum'mawa, zinamera pambuyo pao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 ndipo, taona, ngala zisanu ndi ziwiri zina zofota, zoonda, zopserera ndi mphepo ya kum'mawa, zinamera pambuyo pao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pomwepo padaphukanso ngala zina zatirigu zisanu ndi ziŵiri zofwapa, zopserera ndi mphepo yakuvuma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kenaka panaphukanso ngala zina zisanu ndi ziwiri zofota, zowonda ndi zowauka ndi mphepo ya kummawa. Onani mutuwo |