Genesis 41:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo pamene zinadya sizinadziwike kuti zinadya; koma zinaipabe m'maonekedwe ao monga poyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo pamene zinadya sizinadziwika kuti zinadya; koma zinaipabe m'maonekedwe ao monga poyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma zitadya zinzakezo, palibe ndi mmodzi yemwe akadazindikira, popeza kuti ng'ombe zoondazo sizidasinthike konse kaonekedwe kake, koma zidangokhala zoonda ndithu monga kale. Tsono ndidadzuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma ngakhale ngʼombezi zinadya zinazo, palibe amene akanatha kuzindikira kuti zinatero popeza zinali zosaonekabe bwino monga poyamba. Ndipo ndinadzidzimuka. Onani mutuwo |