Genesis 41:20 - Buku Lopatulika20 ndipo ng'ombe zazikazi zoonda ndi za maonekedwe oipa zinadya ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri zonenepa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 ndipo ng'ombe zazikazi zoonda ndi za maonekedwe oipa zinadya ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri zonenepa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ng'ombe zoondazo zidadya zinzake zonenepa zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ngʼombe zosaoneka bwino ndi zowonda zija zinadya zisanu ndi ziwiri zonenepa zimene zinatuluka poyamba zija. Onani mutuwo |