Genesis 40:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo wopereka chikho wamkulu anafotokozera Yosefe loto lake, nati kwa iye, M'kulota kwanga, taona, mpesa unali pamaso panga: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo wopereka chikho wamkulu anafotokozera Yosefe loto lake, nati kwa iye, M'kulota kwanga, taona, mpesa unali pamaso panga: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Motero uja woperekera vinyoyu adayambapo kunena maloto ake, adati, “Ine ndinalota ndikuwona mtengo wamphesa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Choncho mkulu wa operekera zakumwa uja anamuwuza Yosefe maloto ake. Anati, “Mʼmaloto anga ndinaona mtengo wa mpesa, Onani mutuwo |