Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 40:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo anafunsa akulu a Farao osungidwa naye m'nyumba ya mbuyake, kuti, Nkhope zanu zagwa bwanji lero?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo anafunsa akulu a Farao osungidwa naye m'nyumba ya mbuyake, kuti, Nkhope zanu zagwa bwanji lero?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Adaŵafunsa kuti, “Mwatani mukuwoneka ngati achisoni lero?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Choncho anafunsa akuluakulu a kwa Farao amene anali naye mʼndende muja kuti, “Bwanji nkhope zanu zili zachisoni lero?”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 40:7
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Yosefe analowa kwa iwo m'mawa, nawaona iwo, taonani, anali oziya.


Ndipo anaika onse m'kaidi masiku atatu.


Nanena naye, Iwe mwana wa mfumu, uonderanji tsiku ndi tsiku? Sungandiuze kodi? Ndipo Aminoni anati kwa iye, Ndikonda Tamara, mlongo wa mbale wanga Abisalomu.


Ninena nane mfumu, Nkhope yako nja chisoni chifukwa ninji popeza sudwala? Ichi si chinthu china koma chisoni cha mtima. Pamenepo ndinachita mantha aakulu.


Ndipo anati kwa iwo, Mau awa ndi otani mulandizanawo poyendayenda? Ndipo anaima ndi nkhope zao zachisoni.


Nati iye, Mwanditengera milungu yanga ndinaipanga, ndi wansembe, ndi kuchoka; chinditsaliranso chiyani? Ndipo muneneranji kwa ine, Chakusowa nchiyani?


Ndipo mwamuna wake Elikana anati kwa iye, Hana, umaliriranji? Ndipo umakaniranji kudya? Ndipo mtima wako uwawa ninji? Ine sindili wakuposa ana khumi kwa iwe kodi?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa