Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 40:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo Farao anakwiyira akulu ake awiriwo wamkulu wa opereka chikho, ndi wamkulu wa ophika mkate.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo Farao anakwiyira akulu ake awiriwo wamkulu wa opereka chikho, ndi wamkulu wa ophika mkate.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Farao adaŵakwiyira kwambiri antchito ake aŵiriwo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Farao anapsa mtima ndi akuluakulu awiriwa,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 40:2
11 Mawu Ofanana  

Ndipo panali zitapita izi, wopereka chikho wa mfumu ya Aejipito ndi wophika mkate wake anamchimwira mbuye wao mfumu ya Aejipito.


Ndipo anabwezanso wopereka chikho ku ntchito yake; ndipo iye anapereka chikho m'manja a Farao.


Koma wopereka chikho wamkulu sanakumbukire Yosefe, koma anamuiwala.


Farao anakwiya ndi anyamata ake, nandiika ine ndisungidwe m'nyumba ya kazembe wa alonda, ine ndi wophika mkate wamkulu:


ndi woyang'anira minda yampesa ndiye Simei Mramati; ndi woyang'anira zipatso za minda yampesa zisungike mosungiramo vinyo ndiye Zabidi Msifamu;


Indedi, kuzaza kwake kwa munthu kudzakulemekezani; chotsalira cha kuzazaku mudzachiletsa.


Mkwiyo wa mfumu ndi mithenga ya imfa; wanzeru adzaukhulula.


Mkwiyo wa mfumu ukunga kubangula kwa mkango; koma kukoma mtima kwake kunga mame pamsipu.


Munthu waukali alipire mwini; pakuti ukampulumutsa udzateronso.


Kupweteka mtima nkwa nkhanza, mkwiyo usefuka; koma ndani angalakike ndi nsanje?


Koma Herode anaipidwa nao a ku Tiro ndi Sidoni; ndipo anamdzera iye ndi mtima umodzi, ndipo m'mene adakopa Blasito mdindo wa mfumu, anapempha mtendere, popeza dziko lao linapeza zakudya zochokera ku dziko la mfumu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa