Genesis 40:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo panali zitapita izi, wopereka chikho wa mfumu ya Aejipito ndi wophika mkate wake anamchimwira mbuye wao mfumu ya Aejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo panali zitapita izi, wopereka chikho wa mfumu ya Aejipito ndi wophika mkate wake anamchimwira mbuye wao mfumu ya Aejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Patapita kanthaŵi, munthu woperekera vinyo pamodzi ndi wopanga buledi ku nyumba ya mfumu ya ku Ejipito, adalakwira mbuyao mfumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patapita nthawi, woperekera zakumwa ndi wopanga buledi a ku nyumba kwa mfumu ya ku Igupto analakwira mbuye wawoyo. Onani mutuwo |