Genesis 4:24 - Buku Lopatulika24 Ngati Kaini adzabwezeredwa kasanu ndi kawiri, koma Lameki makumi asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ngati Kaini adzabwezeredwa kasanu ndi kawiri, koma Lameki makumi asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Ngati wopha Kaini amlipsira kasanunkaŵiri, ndiye kuti wopha ine Lameki adzamlipsira kokwanira 77.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ngati wopha Kaini amulipsira kasanu nʼkawiri, ndiye kuti wopha ine Lameki adzamulipsira kokwanira 77.” Onani mutuwo |