Genesis 4:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anati, Wachita chiyani? Mau a mwazi wa mphwako andifuulira Ine kunthaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anati, Wachita chiyani? Mau a mwazi wa mphwako andifuulira Ine kunthaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Chauta adamufunsanso kuti, “Kodi wachita chiyani? Magazi a mng'ono wako akulira kwa Ine kuchokera m'nthaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yehova anati, “Kodi wachita chiyani? Tamvera! Magazi a mʼbale wako akulirira kwa Ine kuchokera mʼnthaka. Onani mutuwo |