Genesis 39:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo panali pamene mkazi anaona kuti anasiya chofunda chake m'dzanja lake, nathawira kubwalo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo panali pamene mkazi anaona kuti anasiya chofunda chake m'dzanja lake, nathawira kubwalo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono mkazi uja ataona kuti Yosefe wasiya mwinjiro ndipo wathaŵira pabwalo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pamene mkazi uja anaona kuti Yosefe wamusiyira mkanjo wake mʼmanja mwake nathawira kunja kwa nyumba, Onani mutuwo |