Genesis 39:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo panali, nthawi yomweyo, iye analowa m'nyumba kuti agwire ntchito yake; ndipo munalibe amuna a m'nyumba m'katimo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo panali, nthawi yomweyo, iye analowa m'nyumba kuti agwire ntchito yake; ndipo munalibe amuna a m'nyumba m'katimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma tsiku lina Yosefe adaloŵa m'nyumba kuti agwire ntchito, ndipo panalibe antchito ena m'nyumbamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsiku lina Yosefe analowa mʼnyumbamo kukagwira ntchito zake, ndipo munalibe wina aliyense wantchito mʼnyumbamo. Onani mutuwo |