Genesis 39:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo pali pakunenanena ndi Yosefe tsiku ndi tsiku, iye sanamvere mkazi kugona naye kapena kukhala naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo pali pakunenanena ndi Yosefe tsiku ndi tsiku, iye sanamvere mkazi kugona naye kapena kukhala naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ngakhale mkazi uja ankalankhula mau ameneŵa kwa Yosefe tsiku ndi tsiku, Yosefeyo sankamvako mpang'ono pomwe, ndipo sankalola kuchita naye zoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo ngakhale kuti iye anayankhula mawu omwewa ndi Yosefe tsiku ndi tsiku, Yosefe sanalole kugona naye ngakhale kukhala naye pafupi. Onani mutuwo |