Genesis 38:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo pambuyo pake anabadwa mbale wake, amene anali ndi chingwe chofiira pamkono pake, dzina lake linatchedwa Zera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo pambuyo pake anabadwa mbale wake, amene anali ndi chingwe chofiira pamkono pake, dzina lake linatchedwa Zera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Pambuyo pake mbale wake adabadwa chingwe chofiira chija chili lende ku dzanja. Tsono iyeyu adatchedwa Zera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Pambuyo pake mʼbale wake amene anali ndi ulusi wofiira pa mkono wake uja anabadwa ndipo anapatsidwa dzina lakuti Zera. Onani mutuwo |