Genesis 38:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo panali pamene anabala kuti mmodzi anatulutsa dzanja; ndipo namwino anatenga chingwe chofiira namanga padzanja lake, kuti, Uyu anayamba kubadwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo panali pamene anabala kuti mmodzi anatulutsa dzanja; ndipo namwino anatenga chingwe chofiira namanga pa dzanja lake, kuti, Uyu anayamba kubadwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Pa nthaŵi yochira, mmodzi mwa anawo adatulutsa dzanja. Mzamba adaligwira, nalimanga ndi chingwe chofiira nati, “Ameneyu ndiye woyamba kubadwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Pamene ankabereka, mmodzi wa iwo anatulutsa dzanja lake. Choncho mzamba anatenga kawulusi kofiira nakamangirira pa mkono pa mwanayo nati, “Uyu ndiye anayamba kubadwa.” Onani mutuwo |