Genesis 38:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo panali nthawi ya kubala kwake, taonani, amapasa anali m'mimba mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo panali nthawi ya kubala kwake, taonani, amapasa anali m'mimba mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Itakwana nthaŵi yakuti Tamara achire, m'mimba mwake munali mapasa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Pamene Tamara nthawi inamukwanira yoti abeleke, mʼmimbamo munali mapasa. Onani mutuwo |