Genesis 38:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo mkazi anauka nachoka, navula chofunda chake, navala zovala zamasiye zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo mkazi anauka nachoka, navula chofunda chake, navala zovala zamasiye zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono Tamara adanyamuka nachokapo. Adachotsa nsalu imene adaadziphimba nayo kumaso ija, navalanso zovala zake zaumasiye zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Kenaka Tamara anachoka, navula nsalu anadziphimba nayo ija, navalanso zovala zake za umasiye zija. Onani mutuwo |