Genesis 38:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo iye anati, Ndidzatumiza kwa iwe kamwana ka mbuzi ka m'ziweto. Ndipo mkazi nati, Kodi udzandipatsa ine chikole mpaka ukatumiza? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo iye anati, Ndidzatumiza kwa iwe kamwana ka mbuzi ka m'ziweto. Ndipo mkazi nati, Kodi udzandipatsa ine chikole mpaka ukatumiza? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Yuda adayankha kuti, “Ndidzakutumizira mbuzi yaing'ono ya m'khola mwanga.” Tsono Tamarayo adati, “Chabwino, ndivomera mukandipatsa chikole choti mpaka mudzanditumizire.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Iye anati, “Ndidzakutumizira kamwana kambuzi ka mʼkhola mwanga.” Mkaziyo anayankha kuti, “Chabwino, ndavomera, koma mungandipatse chikole mpaka mutanditumizira mbuziyo?” Onani mutuwo |