Genesis 38:15 - Buku Lopatulika15 Pamene Yuda anamuona iye, anaganizira kuti ali mkazi wadama: chifukwa iye anabisa nkhope yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pamene Yuda anamuona iye, anaganizira kuti ali mkazi wadama: chifukwa iye anabisa nkhope yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Yuda atamuwona, adaamuyesa mkazi wadama, chifukwa anali atadziphimba kumaso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Yuda atamuona anangomuyesa mkazi wadama chabe, chifukwa anadziphimba nkhope. Onani mutuwo |