Genesis 38:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anamuuza Tamara, kuti, Taona, mpongozi wako akwera kunka ku Timna kuti akasenge nkhosa zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anamuuza Tamara, kuti, Taona, mpongozi wako akwera kunka ku Timna kuti akasenge nkhosa zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Munthu wina adauza Tamara kuti, “Apongozi ako akupita ku Timna kukameta nkhosa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Tamara atamva kuti apongozi ake akupita ku Timna kukameta nkhosa, Onani mutuwo |