Genesis 37:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo anabwera kwa abale ake, nati, Mwana palibe; ndipo ine ndipita kuti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo anabwera kwa abale ake, nati, Mwana palibe; ndipo ine ndipita kuti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Ndipo adabwerera kwa abale ake aja naŵauza kuti, “Mnyamata ujatu palibe! Tsono ine ndichite chiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 nabwerera kwa abale ake nati, “Mnyamata uja mulibemo! Nanga ndilowere kuti ine tsopano?” Onani mutuwo |