Genesis 37:3 - Buku Lopatulika3 Koma Israele anamkonda Yosefe koposa ana ake onse, pakuti anali mwana wa ukalamba wake; ndipo anamsokera iye malaya amwinjiro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Koma Israele anamkonda Yosefe koposa ana ake onse, pakuti anali mwana wa ukalamba wake; ndipo anamsokera iye malaya amwinjiro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Israele ankakonda Yosefe kupambana ana ake ena onse, popeza kuti anali mwana wake wapaukalamba. Adamsokera mkanjo wautali wamanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsono Israeli ankakonda Yosefe koposa ana ake ena onse, chifukwa anali mwana wobadwa muukalamba wake. Ndipo anamusokera mkanjo wa manja aatali. Onani mutuwo |