Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 37:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo Yakobo anakhala m'dziko limene anakhalamo mlendo atate wake, m'dziko la Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo Yakobo anakhala m'dziko limene anakhalamo mlendo atate wake, m'dziko la Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Yakobe adakhalabe ku dziko la Kanani kumene bambo wake ankakhala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Yakobo ankakhala mʼdziko la Kanaani kumene abambo ake ankakhala.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 37:1
6 Mawu Ofanana  

Ndipo ndidzakupatsa iwe ndi mbeu zako za pambuyo pako, dziko la maulendo anu, dziko lonse la Kanani likhale lako nthawi zonse: ndipo Ine ndidzakhala Mulungu wako.


Ine ndine mlendo wakukhala ndi inu: mundipatse ndikhale ndi manda pamodzi ndi inu, kuti ndiike wakufa wanga ndisamthirenso maso.


akupatse iwe mdalitso wa Abrahamu, iwe ndi mbeu zako pamodzi nawe: kuti ulowe m'dziko limene ukhalamo mlendo, limene Mulungu anampatsa Abrahamu.


mfumu Magadiele, mfumu Iramu; amenewa ndi mafumu a Edomu, monga mwa kukhala kwao m'dziko lokhala laolao. Uyo ndiye Esau atate wao wa Aedomu.


Chifukwa chuma chao chinali chambiri chotero kuti sanakhoze kukhala pamodzi; ndipo dziko lokhalamo iwo silinakhoze kuwakwanira chifukwa cha ng'ombe zao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa