Genesis 36:5 - Buku Lopatulika5 ndipo Oholibama anabala Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora; amenewa ndi ana aamuna a Esau, amene anambadwira m'dziko la Kanani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndipo Oholibama anabala Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora; amenewa ndi ana amuna a Esau, amene anambadwira m'dziko la Kanani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 ndipo Oholibama adabala Yeusi, Yalamu ndi Kora. Ameneŵa ndi ana amene adabereka Esau m'dziko la Kanani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 ndipo Oholibama anabereka Yeusi, Yolamu ndi Kora. Amenewa anali ana a Esau amene anabadwira ku Kanaani. Onani mutuwo |