Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 36:13 - Buku Lopatulika

13 Ndi ana aamuna a Reuwele: Nahati, ndi Zera, Sama, ndi Miza; amenewa ndi ana a Basemati mkazi wake wa Esau.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndi ana amuna a Reuwele: Nahati, ndi Zera, Sama, ndi Miza; amenewa ndi ana a Basemati mkazi wake wa Esau.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ana a Reuele ndi aŵa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Ameneŵa ndiwo ana a Basemati mkazi wa Esau.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Awa ndi ana a Reueli: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Amenewa ndi ana a Basemati, mkazi wa Esau.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:13
5 Mawu Ofanana  

Pamene Esau anali wa zaka makumi anai, anakwatira Yuditi mwana wamkazi wa Beeri Muhiti, ndi Basemati mwana wamkazi wa Eloni Muhiti.


Ndipo Timna anali mkazi wake wamng'ono wa Elifazi mwana wamwamuna wa Esau; ndipo anambalira Elifazi Amaleke: amenewa ndi ana aamuna a Ada mkazi wake wa Esau.


Ana aamuna a Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni, mkazi wake wa Esau, ndi awa: ndipo iye anambalira Esau Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora.


Amenewa ndi ana aamuna a Reuwele mwana wamwamuna wa Esau: mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Sama, mfumu Miza; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Reuwele m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana aamuna a Basemati mkazi wake wa Esau.


Ana a Reuwele: Nahati, Zera, Sama, ndi Miza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa