Genesis 36:14 - Buku Lopatulika14 Ana aamuna a Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni, mkazi wake wa Esau, ndi awa: ndipo iye anambalira Esau Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ana amuna a Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni, mkazi wake wa Esau, ndi awa: ndipo iye anambalira Esau Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ana a Oholibama mkazi wa Esau ndi aŵa: Yeusi, Yalamu ndi Kora. Oholibamayo anali mwana wa Ana mwana wa Zibiyoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ana aamuna a Oholibama, mkazi wa Esau, mwana wa Ana ndi mdzukulu wa Zebeoni ndi awa: Yeusi, Yolamu ndi Kora. Onani mutuwo |