Genesis 35:3 - Buku Lopatulika3 tinyamuke, tikwere tinke ku Betele: ndipo tidzamanga kumeneko guwa la nsembe la Mulungu amene anandivomereza tsiku la mavuto anga, ndiponso anali ndi ine m'njira m'mene ndinapitamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 tinyamuke, tikwere tinke ku Betele: ndipo tidzamanga kumeneko guwa la nsembe la Mulungu amene anandivomereza tsiku la mavuto anga, ndiponso anali ndi ine m'njira m'mene ndinapitamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tichokako kuno, tipita ku Betele kumene ndikamange guwa la Mulungu amene adandithandiza pa nthaŵi ya mavuto anga. Ndiye ndithu amene wakhala nane kulikonse komwe ndinkapita.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tiyeni tinyamuke kuchoka kuno kupita ku Beteli. Kumeneko ndikamumangira guwa lansembe Mulungu amene anandithandiza pa nthawi za masautso anga, komanso amene wakhala nane mʼmayendedwe anga onse.” Onani mutuwo |