Genesis 32:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo anati, Dzina lako silidzatchedwanso Yakobo, koma Israele, chifukwa unayesana naye Mulungu ndithu, ndipo unapambana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo anati, Dzina lako silidzatchedwanso Yakobo, koma Israele, chifukwa unayesana naye Mulungu ndithu, ndipo unapambana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Munthu uja adati, “Dzina lako silidzakhalanso Yakobe. Walimbana ndi Mulungu ndi anthu, ndipo wapambana. Motero dzina lako lidzakhala Israele.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Pamenepo munthuyo anati, “Dzina lako silidzakhalanso Yakobo koma Israeli, chifukwa walimbana ndi Mulungu ndi anthu ndipo wapambana.” Onani mutuwo |