Genesis 32:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo pamene anaona kuti sanamgonjetse, anakhudza nsukunyu ya ntchafu yake; ndipo nsukunyu ya ntchafu yake ya Yakobo inaguluka, pakulimbana naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo pamene anaona kuti sanamgonjetsa, anakhudza nsukunyu ya ntchafu yake; ndipo nsukunyu ya ntchafu yake ya Yakobo inaguluka, pakulimbana naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Munthuyo ataona kuti sakuphulapo kanthu, adamenya Yakobe m'nyung'unyu, nyung'unyuyo nkuguluka polimbanapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pamene munthuyo anaona kuti sangathe kumugonjetsa, anakhudza nyungʼunyu ya pa ntchafu ya Yakobo ndipo inaguluka polimbanapo. Onani mutuwo |